Ezekieli 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wogulitsa sadzabwerera pamalo amene anagulitsa ngakhale atadzapulumuka, chifukwa zinthu zonse zimene zili mʼmasomphenyawo zidzachitikira anthu onse. Palibe amene adzabwerere, ndipo chifukwa cha zolakwa zake,* palibe amene adzapulumutse moyo wake. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:13 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 13
13 Wogulitsa sadzabwerera pamalo amene anagulitsa ngakhale atadzapulumuka, chifukwa zinthu zonse zimene zili mʼmasomphenyawo zidzachitikira anthu onse. Palibe amene adzabwerere, ndipo chifukwa cha zolakwa zake,* palibe amene adzapulumutse moyo wake.