Ezekieli 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ine ndidzayangʼana kumbali kuti ndisawaone+ ndipo adzaipitsa malo anga opatulika.* Akuba adzalowa mʼmalowo nʼkuwaipitsa.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:22 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 13
22 Ine ndidzayangʼana kumbali kuti ndisawaone+ ndipo adzaipitsa malo anga opatulika.* Akuba adzalowa mʼmalowo nʼkuwaipitsa.+