Ezekieli 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Anthu akadzayamba kuvutika, azidzafunafuna mtendere koma sadzaupeza.+