26 Mʼdzikolo mudzakhala mavuto otsatizanatsatizana ndipo muzidzamveka mauthenga otsatizanatsatizana. Anthu azidzafuna kumva masomphenya kuchokera kwa mneneri.+ Koma wansembe sadzathanso kuphunzitsa malamulo aphindu ndipo anthu achikulire sadzaperekanso malangizo othandiza.+