Ezekieli 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno iye anauza amuna ena aja ine ndikumva, kuti: “Mʼtsatireni ameneyu. Muyendeyende mumzindamo nʼkumapha anthu. Diso lanu lisamve chisoni ndipo musasonyeze aliyense chifundo.+
5 Ndiyeno iye anauza amuna ena aja ine ndikumva, kuti: “Mʼtsatireni ameneyu. Muyendeyende mumzindamo nʼkumapha anthu. Diso lanu lisamve chisoni ndipo musasonyeze aliyense chifundo.+