-
Ezekieli 9:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kenako ndinaona munthu amene anavala zovala zansalu uja, yemwe mʼchiuno mwake munali kachikwama konyamuliramo inki ndi zolembera atabwera, ndipo ananena kuti: “Ndachita zonse zimene munandilamula.”
-