-
Ezekieli 10:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Kenako Mulungu analamula munthu amene anavala zovala zansalu uja kuti: “Tenga moto pakati pa mawilo, pakati pa akerubi.” Ndipo munthuyo anapita nʼkukaima pambali pa wilo.
-