Ezekieli 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno mmodzi wa akerubiwo anatambasulira dzanja lake pamoto umene unali pakati pa akerubiwo.+ Iye anatenga motowo pangʼono nʼkuuika mʼmanja mwa munthu amene anavala zovala zansalu uja+ ndipo munthuyo anautenga nʼkuchoka.
7 Ndiyeno mmodzi wa akerubiwo anatambasulira dzanja lake pamoto umene unali pakati pa akerubiwo.+ Iye anatenga motowo pangʼono nʼkuuika mʼmanja mwa munthu amene anavala zovala zansalu uja+ ndipo munthuyo anautenga nʼkuchoka.