Ezekieli 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Amenewa anali angelo amene ndinawaona pansi pa mpando wachifumu wa Mulungu wa Isiraeli kumtsinje wa Kebara,+ choncho ndinadziwa kuti anali akerubi.
20 Amenewa anali angelo amene ndinawaona pansi pa mpando wachifumu wa Mulungu wa Isiraeli kumtsinje wa Kebara,+ choncho ndinadziwa kuti anali akerubi.