Ezekieli 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Maonekedwe a nkhope zawo anali ofanana ndi a nkhope zimene ndinaziona mʼmphepete mwa mtsinje wa Kebara.+ Mngelo aliyense ankapita kutsogolo basi.+
22 Maonekedwe a nkhope zawo anali ofanana ndi a nkhope zimene ndinaziona mʼmphepete mwa mtsinje wa Kebara.+ Mngelo aliyense ankapita kutsogolo basi.+