Ezekieli 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako mzimu unandinyamula nʼkupita nane kugeti la nyumba ya Yehova limene linayangʼana kumʼmawa.+ Pakhomo la getilo ndinaonapo amuna 25 omwe anali akalonga+ ndipo pakati pawo panali Yaazaniya mwana wa Azuri ndi Pelatiya mwana wa Benaya. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:1 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 15
11 Kenako mzimu unandinyamula nʼkupita nane kugeti la nyumba ya Yehova limene linayangʼana kumʼmawa.+ Pakhomo la getilo ndinaonapo amuna 25 omwe anali akalonga+ ndipo pakati pawo panali Yaazaniya mwana wa Azuri ndi Pelatiya mwana wa Benaya.