-
Ezekieli 11:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndiyeno Mulungu anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, amuna amenewa ndi amene akukonza chiwembu ndiponso amene akupereka malangizo oipa mumzindawu.
-