Ezekieli 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo akunena kuti: ‘Ino ndi nthawi yomanga nyumba.+ Mzindawu* uli ngati mphika*+ ndipo ifeyo tili ngati nyama mumphikamo.’ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:3 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, tsa. 89/15/1988, tsa. 15
3 Iwo akunena kuti: ‘Ino ndi nthawi yomanga nyumba.+ Mzindawu* uli ngati mphika*+ ndipo ifeyo tili ngati nyama mumphikamo.’