Ezekieli 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako mzimu wa Yehova unafika pa ine+ ndipo iye anandiuza kuti: “Unene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Inu anthu a nyumba ya Isiraeli, zimene mwanena ndi zoona ndipo ine ndikudziwa zimene mukuganiza.
5 Kenako mzimu wa Yehova unafika pa ine+ ndipo iye anandiuza kuti: “Unene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Inu anthu a nyumba ya Isiraeli, zimene mwanena ndi zoona ndipo ine ndikudziwa zimene mukuganiza.