Ezekieli 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Anthu akufa amene mwawamwaza mumzindawu ndi amene ali nyama ndipo mzindawu ndi mphika.+ Koma inuyo mudzatulutsidwa mumzindawu.’”
7 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Anthu akufa amene mwawamwaza mumzindawu ndi amene ali nyama ndipo mzindawu ndi mphika.+ Koma inuyo mudzatulutsidwa mumzindawu.’”