-
Ezekieli 11:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kwa inu, mzindawu sudzakhala mphika ndipo inuyo simudzakhala nyama mkati mwa mphikawo. Ndidzakuweruzirani mʼmalire a Isiraeli.
-