Ezekieli 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inuyo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, chifukwa simunasunge malamulo anga ndiponso simunatsatire zigamulo zanga.+ Koma inu munatsatira zigamulo za mitundu ya anthu amene akuzungulirani.’”+
12 Inuyo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, chifukwa simunasunge malamulo anga ndiponso simunatsatire zigamulo zanga.+ Koma inu munatsatira zigamulo za mitundu ya anthu amene akuzungulirani.’”+