Ezekieli 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nditangomaliza kulosera, Pelatiya mwana wa Benaya anamwalira. Choncho ine ndinagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yanga pansi, nʼkufuula kuti: “Mayo ine, inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kodi mukufuna kuwononga Aisiraeli amene atsalawa?”+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:13 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, ptsa. 8-9
13 Nditangomaliza kulosera, Pelatiya mwana wa Benaya anamwalira. Choncho ine ndinagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yanga pansi, nʼkufuula kuti: “Mayo ine, inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kodi mukufuna kuwononga Aisiraeli amene atsalawa?”+