-
Ezekieli 11:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Choncho uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ngakhale kuti ndawachotsa nʼkuwapititsa kutali kuti azikakhala pakati pa mitundu yosiyanasiyana ya anthu ndipo ndawabalalitsira mʼmayiko osiyanasiyana,+ ine ndidzakhala malo opatulika kwa iwo kwa kanthawi kochepa, kumayiko amene iwo apitako.”’”+
-