Ezekieli 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mtsogoleri amene ali pakati pawo adzanyamula katundu wake paphewa nʼkuchoka kuli mdima. Adzabowola khoma nʼkutulutsirapo katundu wake.+ Iye adzaphimba nkhope kuti asaone pansi.
12 Mtsogoleri amene ali pakati pawo adzanyamula katundu wake paphewa nʼkuchoka kuli mdima. Adzabowola khoma nʼkutulutsirapo katundu wake.+ Iye adzaphimba nkhope kuti asaone pansi.