-
Ezekieli 12:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Anthu amʼdzikoli uwauze kuti, ‘Izi nʼzimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kwa anthu amene akukhala mu Yerusalemu, mʼdziko la Isiraeli: “Iwo adzadya chakudya chawo ali ndi nkhawa ndipo adzamwa madzi ali ndi mantha aakulu. Izi zidzachitika chifukwa dziko lawo lidzakhala bwinja lokhalokha+ chifukwa cha zinthu zachiwawa zimene anthu onse amene akukhala mmenemo akuchita.+
-