-
Ezekieli 12:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Choncho uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘Palibe mawu aliwonse omwe ndalankhula amene sadzachitika pa nthawi yake. Zonse zimene ndanena zidzachitika,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’”
-