Ezekieli 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Simudzapita mʼmalo ogumuka a mipanda yamiyala kuti mukamangirenso nyumba ya Isiraeli+ malo amene anagumukawo, nʼcholinga choti Aisiraeli adzapulumuke pa nkhondo pa tsiku la Yehova.”+
5 Simudzapita mʼmalo ogumuka a mipanda yamiyala kuti mukamangirenso nyumba ya Isiraeli+ malo amene anagumukawo, nʼcholinga choti Aisiraeli adzapulumuke pa nkhondo pa tsiku la Yehova.”+