-
Ezekieli 13:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Khoma limene mwalipaka laimulo, ndidzaligwetsa pansi ndipo maziko ake adzaonekera. Mzindawo ukamadzawonongedwa, inuyo mudzafera momwemo. Ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.
-