Ezekieli 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndikadzasonyeza mkwiyo wanga wonse pakhomalo ndiponso pa anthu amene analipaka laimuwo, ndidzakuuzani kuti: “Khoma lija kulibe komanso anthu amene analipaka laimu aja kulibenso.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:15 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, ptsa. 8-9
15 Ndikadzasonyeza mkwiyo wanga wonse pakhomalo ndiponso pa anthu amene analipaka laimuwo, ndidzakuuzani kuti: “Khoma lija kulibe komanso anthu amene analipaka laimu aja kulibenso.+