-
Ezekieli 13:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Koma iwe mwana wa munthu, yangʼana ana aakazi a anthu a mtundu wako, amene akulosera zamʼmutu mwawo ndipo ulosere zoipa zimene zidzawachitikire.
-