-
Ezekieli 13:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Akazi inu, ine ndikudana ndi zinthu zanu zovala mʼmikono, zimene mukuzigwiritsa ntchito potchera anthu msampha ngati kuti ndi mbalame. Ndizichotsa mʼmikono mwanu nʼkumasula anthu amene mwawatchera msampha ngati mbalame.
-