Ezekieli 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndingʼamba nsalu zanu zophimba kumutu ndi kulanditsa anthu anga mʼmanja mwanu. Iwo sadzakhalanso ngati zinthu zoti muzidzazisaka nʼkuzigwira ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.+
21 Ndingʼamba nsalu zanu zophimba kumutu ndi kulanditsa anthu anga mʼmanja mwanu. Iwo sadzakhalanso ngati zinthu zoti muzidzazisaka nʼkuzigwira ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.+