Ezekieli 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu mwakhumudwitsa munthu wolungama chifukwa cha chinyengo chanu,+ pamene ineyo sindinafune kuti azivutika.* Ndipo mwalimbitsa manja a munthu woipa+ kuti asasiye njira zake zoipazo. Chifukwa cha zimenezi iye sadzapitiriza kukhala ndi moyo.+
22 Inu mwakhumudwitsa munthu wolungama chifukwa cha chinyengo chanu,+ pamene ineyo sindinafune kuti azivutika.* Ndipo mwalimbitsa manja a munthu woipa+ kuti asasiye njira zake zoipazo. Chifukwa cha zimenezi iye sadzapitiriza kukhala ndi moyo.+