-
Ezekieli 14:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Choncho ulankhule nawo ndipo uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ngati munthu aliyense mu Isiraeli watsimikiza mumtima mwake kuti azitsatira mafano ake onyansa nʼkuika chinthu chopunthwitsa chimene chachititsa kuti anthu achite tchimo kenako nʼkukafunsira kwa mneneri, ine Yehova ndidzamuyankha moyenera, mogwirizana ndi kuchuluka kwa mafano ake onyansa.
-