Ezekieli 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Bwererani, musiye kutsatira mafano anu onyansa ndipo musiye zinthu zonse zonyansa zimene mukuchita.+
6 Choncho uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Bwererani, musiye kutsatira mafano anu onyansa ndipo musiye zinthu zonse zonyansa zimene mukuchita.+