-
Ezekieli 14:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ngati munthu aliyense amene akukhala mu Isiraeli, kaya ndi mbadwa kapena mlendo, wasiya kunditsatira ndipo watsimikiza mumtima mwake kuti azitsatira mafano ake onyansa nʼkuika chinthu chopunthwitsa chimene chachititsa kuti anthu achite tchimo kenako nʼkukafunsira kwa mneneri wanga,+ ine Yehova ndidzamuyankha ndekha.
-