Ezekieli 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kuti a nyumba ya Isiraeli asadzasiyenso kunditsatira nʼkumangoyendayenda ndiponso kuti asiye kudziipitsa ndi zolakwa zawo zonse. Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
11 kuti a nyumba ya Isiraeli asadzasiyenso kunditsatira nʼkumangoyendayenda ndiponso kuti asiye kudziipitsa ndi zolakwa zawo zonse. Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”