-
Ezekieli 14:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 pali ine Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘ngakhale zikanakhala kuti amuna atatu amenewa ali mʼdzikolo, iwo sakanapulumutsa ana awo aamuna kapena aakazi. Iwo okhawo ndi amene akanapulumuka ndipo dzikolo likanakhala bwinja.’”
-