-
Ezekieli 14:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 pali ine Mulungu wamoyo, akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘ngakhale zikanakhala kuti amuna atatu amenewa ali mʼdzikolo, iwo sakanapulumutsa ana awo aamuna kapena aakazi. Iwo okhawo ndi amene akanapulumuka.’”
-