Ezekieli 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Zidzakhalanso choncho ndikadzabweretsa zilango zanga* 4+ izi: lupanga, njala, zilombo zolusa zakutchire ndi mliri+ kuti zikaphe anthu ndi ziweto mu Yerusalemu.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:21 Nsanja ya Olonda,10/15/1988, tsa. 11
21 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Zidzakhalanso choncho ndikadzabweretsa zilango zanga* 4+ izi: lupanga, njala, zilombo zolusa zakutchire ndi mliri+ kuti zikaphe anthu ndi ziweto mu Yerusalemu.+