Ezekieli 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo adzakutonthozani mukadzaona njira zawo ndi zochita zawo. Ndipo mudzadziwa kuti zonse zimene ndinachitira mzindawo, sindinazichite popanda chifukwa,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
23 Iwo adzakutonthozani mukadzaona njira zawo ndi zochita zawo. Ndipo mudzadziwa kuti zonse zimene ndinachitira mzindawo, sindinazichite popanda chifukwa,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”