-
Ezekieli 16:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ine ndikudutsa pafupi ndinakuona ukuponyaponya timiyendo tako mʼmwamba uli magazi okhaokha. Ndiyeno utagona pansi ndiponso uli ndi magazi okhaokha ndinakuuza kuti, ‘Ukhala ndi moyo!’ Ndithu ndinakuuza uli magazi okhaokha kuti, ‘Ukhala ndi moyo!’
-