-
Ezekieli 16:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndinakupangitsa kuti ukhale gulu lalikulu la anthu ngati mbewu zimene zaphuka mʼmunda. Unakula nʼkukhala mtsikana ndipo unkavala zodzikongoletsera zabwino kwambiri. Mabere ako anakula ndipo tsitsi lako linatalika, koma unali udakali wosavala ndiponso wamaliseche.”’
-