39 Ndidzakupereka mʼmanja mwa anthu okuukira ndipo iwo adzagwetsa malo ako olambirirako milungu yabodza ndi malo ako okwera.+ Iwo adzakuvula zovala+ ndipo adzatenga zinthu zako zodzikongoletsera zamtengo wapatali+ nʼkukusiya wosavala komanso wamaliseche.