-
Ezekieli 16:52Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
52 Tsopano iweyo ukuyenera kuchita manyazi chifukwa waikira kumbuyo makhalidwe a azichemwali ako. Iwowo ndi olungama kuposa iweyo chifukwa cha tchimo lako lochita zinthu zonyansa kwambiri kuposa zimene iwowo anachita. Choncho uchite manyazi ndi kunyozeka chifukwa chakuti wachititsa kuti azichemwali ako aoneke ngati olungama.’
-