Ezekieli 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chiwombankhangacho chinathyola nsonga yapamwamba penipeni pa nthambi za mtengowo nʼkupita nayo kudziko la anthu ochita malonda.* Kumeneko chinakadzala nsonga ya mkungudzayo mumzinda umene munali anthu ochita malonda.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:4 Nsanja ya Olonda,7/1/2007, ptsa. 12-139/15/1988, tsa. 17
4 Chiwombankhangacho chinathyola nsonga yapamwamba penipeni pa nthambi za mtengowo nʼkupita nayo kudziko la anthu ochita malonda.* Kumeneko chinakadzala nsonga ya mkungudzayo mumzinda umene munali anthu ochita malonda.+