Ezekieli 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako chinatenga mbewu imodzi mwa mbewu zamʼdzikomo+ nʼkuidzala mʼmunda wachonde. Chinadzala mbewuyo mʼmphepete mwa madzi ambiri kuti ikule ngati mtengo wa msondodzi. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:5 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 17
5 Kenako chinatenga mbewu imodzi mwa mbewu zamʼdzikomo+ nʼkuidzala mʼmunda wachonde. Chinadzala mbewuyo mʼmphepete mwa madzi ambiri kuti ikule ngati mtengo wa msondodzi.