Ezekieli 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mbewuyo inamera nʼkukhala mtengo wa mpesa+ waufupi wamasamba ambiri. Nthambi za mtengowo sizinkakulira mʼmbali ndipo mizu yake inali pansi pa nthambizo. Choncho mbewuyo inakhala mtengo wa mpesa ndipo inaphuka nʼkuchita nthambi.+
6 Mbewuyo inamera nʼkukhala mtengo wa mpesa+ waufupi wamasamba ambiri. Nthambi za mtengowo sizinkakulira mʼmbali ndipo mizu yake inali pansi pa nthambizo. Choncho mbewuyo inakhala mtengo wa mpesa ndipo inaphuka nʼkuchita nthambi.+