-
Ezekieli 17:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Kenako kunabwera chiwombankhanga china chachikulu+ chamapiko akuluakulu komanso nthenga zikuluzikulu.+ Ndiyeno mwamsanga, mtengo wa mpesawo unatambasula mizu yake kupita kumene kunali chiwombankhangacho kutali ndi malo amene unadzalidwa. Mtengo wa mpesawo unatambasula nthambi zake kukafika pamene panali chiwombankhangacho kuti chiuthirire.+
-