Ezekieli 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Chonde, uza anthu opandukawo kuti, ‘Kodi simukuzindikira tanthauzo la zinthu zimenezi?’ Auze kuti, ‘Mfumu ya Babulo inabwera ku Yerusalemu nʼkudzatenga mfumu ndi akalonga amumzindawo nʼkupita nawo ku Babulo.+
12 “Chonde, uza anthu opandukawo kuti, ‘Kodi simukuzindikira tanthauzo la zinthu zimenezi?’ Auze kuti, ‘Mfumu ya Babulo inabwera ku Yerusalemu nʼkudzatenga mfumu ndi akalonga amumzindawo nʼkupita nawo ku Babulo.+