Ezekieli 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ‘Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo, ndidzamulanga chifukwa chonyoza lumbiro langa+ ndiponso chifukwa chophwanya pangano langa. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:19 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 17
19 ‘Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo, ndidzamulanga chifukwa chonyoza lumbiro langa+ ndiponso chifukwa chophwanya pangano langa.