Ezekieli 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye sadya zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano mʼmapiri+ komanso sadalira mafano onyansa* a nyumba ya Isiraeli. Iye sagona ndi mkazi wa mnzake+ kapena kugona ndi mkazi amene akusamba.+
6 Iye sadya zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano mʼmapiri+ komanso sadalira mafano onyansa* a nyumba ya Isiraeli. Iye sagona ndi mkazi wa mnzake+ kapena kugona ndi mkazi amene akusamba.+