-
Ezekieli 18:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Sazunza munthu aliyense. Satenga chikole ndipo salanda chilichonse mwauchifwamba. Munthu wanjala amamupatsa chakudya ndipo munthu wamaliseche amamuphimba ndi chovala.
-