-
Ezekieli 18:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma popeza kuti bambo akewo ankachita zachinyengo, ankabera mʼbale wawo mwauchifwamba ndipo ankachita zinthu zoipa pakati pa anthu a mtundu wawo, iwo adzafa chifukwa cha zolakwa zawo.
-